Zikuti bwanji za akuluwa?

 Wosewera wakale wa timu ya Kamuzu Barracks yemwenso ndi msilikali, Diof Simaone,amugamula kukakhala ku ndende zaka makumi awiri (20) kaamba kogonana ndi mwana wa zaka khumi ndi zisanu (15).

Senior Resident Magistrate, Brecious Kondowe, ndiamene wapereka chigamulochi mu nzinda wa Lilongwe.

Kondowe wati wapereka chigamulo chokhwima pofuna kuti a dindo a nchitidwewu atengere phunziro kamba koti palibe amene ali pamwamba pa lamulo.



3 Comments

  1. Zachitika basi. Analakwitsa kusiya kuoereka thandizo sibwenzi zitaululika kkkk

    Komabe zachitika ngakhale chilango chakula

    ReplyDelete
Previous Post Next Post